Salimo 36:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pitirizani kusonyeza chikondi chanu chokhulupirika kwa anthu amene amakudziwani,+Ndiponso chilungamo chanu kwa anthu owongoka mtima.+ Salimo 73:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 73 Mulungu ndi wabwinodi kwa Isiraeli, kwa anthu oyera mtima.+
10 Pitirizani kusonyeza chikondi chanu chokhulupirika kwa anthu amene amakudziwani,+Ndiponso chilungamo chanu kwa anthu owongoka mtima.+