Salimo 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mulungu ndi chishango changa,+ Mpulumutsi wa anthu owongoka mtima.+ Salimo 97:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kuwala kwaunikira olungama+Ndipo owongoka mtima akusangalala.