Salimo 86:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu,+Palibe aliyense amene wachita zinthu zofanana ndi zimene inu mwachita.+ Yesaya 45:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndine Yehova ndipo palibenso wina. Palibenso Mulungu wina kupatulapo ine.+ Ndidzakupatsa mphamvu* ngakhale kuti sukundidziwa,
8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu,+Palibe aliyense amene wachita zinthu zofanana ndi zimene inu mwachita.+
5 Ine ndine Yehova ndipo palibenso wina. Palibenso Mulungu wina kupatulapo ine.+ Ndidzakupatsa mphamvu* ngakhale kuti sukundidziwa,