Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Choncho Hamani anamupachika pamtengo umene anakonzera Moredikayi, ndipo mkwiyo wa mfumu unatha.

  • Salimo 7:14, 15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Taonani munthu amene ali ndi pakati pa zinthu zoipa,

      Watenga pakati pa mavuto ndipo adzabereka mabodza.+

      15 Iye wakumba dzenje ndipo walizamitsa,

      Koma adzagwera mʼdzenje limene wakumba yekhalo.+

  • Salimo 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mitundu ya anthu yagwera mʼdzenje limene anakumba okha.

      Phazi lawo lakodwa mu ukonde umene anatchera okha.+

  • Salimo 57:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Iwo atchera ukonde kuti akole mapazi anga.+

      Ndili ndi nkhawa yaikulu.+

      Anakumba dzenje panjira yanga,

      Koma agweramo okha.+ (Selah)

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena