Salimo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,Pamene ndikukweza manja anga, nditayangʼana kumene kuli chipinda chamkati chamʼmalo anu opatulika.+ Salimo 141:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 141 Inu Yehova, ine ndakuitanani.+ Bwerani mofulumira kuti mudzandithandize.+ Mutchere khutu ndikamakuitanani.+
2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,Pamene ndikukweza manja anga, nditayangʼana kumene kuli chipinda chamkati chamʼmalo anu opatulika.+
141 Inu Yehova, ine ndakuitanani.+ Bwerani mofulumira kuti mudzandithandize.+ Mutchere khutu ndikamakuitanani.+