Salimo 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndathawira kwa inu Yehova.+ Musalole kuti ndichite manyazi.+ Ndipulumutseni chifukwa cha chilungamo chanu.+
31 Ndathawira kwa inu Yehova.+ Musalole kuti ndichite manyazi.+ Ndipulumutseni chifukwa cha chilungamo chanu.+