Yesaya 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa Yehova ndi Woweruza wathu,+Yehova ndi Wotipatsa Malamulo,+Yehova ndi Mfumu yathu.+Iye ndi amene adzatipulumutse.+ Chivumbulutso 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo ankanena kuti: “Tikukuthokozani inu Yehova,* Mulungu Wamphamvuyonse, inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu zanu zazikulu nʼkuyamba kulamulira monga mfumu.+
22 Chifukwa Yehova ndi Woweruza wathu,+Yehova ndi Wotipatsa Malamulo,+Yehova ndi Mfumu yathu.+Iye ndi amene adzatipulumutse.+
17 Iwo ankanena kuti: “Tikukuthokozani inu Yehova,* Mulungu Wamphamvuyonse, inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu zanu zazikulu nʼkuyamba kulamulira monga mfumu.+