Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:26, 27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndiyeno ana anu akadzakufunsani kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani timachita mwambo umenewu?’+ 27 mudzawauze kuti, ‘Umenewu ndi mwambo wopereka nsembe ya Pasika kwa Yehova, amene anadumpha nyumba za Aisiraeli mu Iguputo pamene ankapha Aiguputo ndi mliri, koma anapulumutsa mabanja athu.’”

      Atatero, anthuwo anagwada nʼkuweramira pansi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena