Salimo 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zinthu zakumwamba zikulengeza ulemerero wa Mulungu.+Ndipo mumlengalenga mukufotokoza ntchito ya manja ake.+
19 Zinthu zakumwamba zikulengeza ulemerero wa Mulungu.+Ndipo mumlengalenga mukufotokoza ntchito ya manja ake.+