Salimo 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Imbani nyimbo zotamanda Yehova, inu okhulupirika ake,+Yamikani dzina* lake loyera.+ Aheberi 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu kudzera mwa Yesu.+ Kuchita zimenezi kuli ngati nsembe imene tikupereka kwa Mulungu ndipo timagwiritsa ntchito milomo yathu+ polengeza dzina lake.+
4 Imbani nyimbo zotamanda Yehova, inu okhulupirika ake,+Yamikani dzina* lake loyera.+ Aheberi 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu kudzera mwa Yesu.+ Kuchita zimenezi kuli ngati nsembe imene tikupereka kwa Mulungu ndipo timagwiritsa ntchito milomo yathu+ polengeza dzina lake.+
15 Tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu kudzera mwa Yesu.+ Kuchita zimenezi kuli ngati nsembe imene tikupereka kwa Mulungu ndipo timagwiritsa ntchito milomo yathu+ polengeza dzina lake.+