Salimo 146:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova adzakhala Mfumu kwamuyaya,+Mulungu wako, iwe Ziyoni, adzakhala Mfumu ku mibadwomibadwo. Tamandani Ya!* 1 Timoteyo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kwa Mulungu yekhayo+ yemwe ndi Mfumu yamuyaya,+ amene saafa+ komanso wosaoneka,+ kukhale ulemu ndi ulemerero mpaka kalekale. Ame.
10 Yehova adzakhala Mfumu kwamuyaya,+Mulungu wako, iwe Ziyoni, adzakhala Mfumu ku mibadwomibadwo. Tamandani Ya!*
17 Kwa Mulungu yekhayo+ yemwe ndi Mfumu yamuyaya,+ amene saafa+ komanso wosaoneka,+ kukhale ulemu ndi ulemerero mpaka kalekale. Ame.