Genesis 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndapereka zomera zonse kuti zikhale chakudya+ cha nyama iliyonse yamʼtchire padziko lapansi, chamoyo chilichonse chouluka mumlengalenga komanso chokwawa chilichonse chapadziko lapansi chimene chili ndi moyo.” Ndipo zinaterodi. Salimo 136:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Amapereka chakudya kwa zamoyo zonse,+Chifukwa chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.
30 Ndapereka zomera zonse kuti zikhale chakudya+ cha nyama iliyonse yamʼtchire padziko lapansi, chamoyo chilichonse chouluka mumlengalenga komanso chokwawa chilichonse chapadziko lapansi chimene chili ndi moyo.” Ndipo zinaterodi.
25 Amapereka chakudya kwa zamoyo zonse,+Chifukwa chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.