Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 104:27, 28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Zonsezi zimayembekezera inu

      Kuti muzipatse chakudya pa nyengo yake.+

      28 Zimasonkhanitsa zimene mwazipatsa.+

      Mukatambasula dzanja lanu, zimakhutira ndi zinthu zabwino.+

  • Salimo 107:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Chifukwa iye wathetsa ludzu la anthu aludzu

      Ndipo anthu anjala wawadyetsa zinthu zabwino.+

  • Salimo 132:14, 15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Awa ndi malo anga okhalamo mpaka kalekale.

      Ndidzakhala mmenemu,+ chifukwa zimenezi ndi zimene ndikulakalaka.

      15 Ndidzadalitsa kwambiri malo amenewa ndi chakudya.

      Anthu ake osauka ndidzawapatsa chakudya chokwanira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena