Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 9:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Chifukwa amoyo amadziwa kuti adzafa,+ koma akufa sadziwa chilichonse+ komanso salandira mphoto iliyonse,* chifukwa zonse zimene anthu akanawakumbukira nazo zimaiwalika.+

  • Mlaliki 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chilichonse chimene dzanja lako lapeza kuti lichite, uchichite ndi mphamvu zako zonse, chifukwa ku Manda*+ kumene ukupitako kulibe kugwira ntchito, kuganiza zochita, kudziwa zinthu kapena nzeru.

  • Yesaya 38:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chifukwa Manda* sangakupatseni ulemerero,+

      Imfa singakutamandeni.+

      Anthu amene akutsikira kudzenje sangayembekezere kuti muwasonyeze kukhulupirika kwanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena