-
Salimo 142:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Nditulutseni mundende yamdima
Kuti nditamande dzina lanu.
Anthu olungama andizungulire
Chifukwa mumandichitira zabwino.
-