Salimo 142:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nditulutseni mundende ya mdima+Kuti nditamande dzina lanu.+Chititsani kuti anthu olungama asonkhane ndi kundizungulira,+Chifukwa mumandichitira zabwino.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 142:7 Nsanja ya Olonda,3/15/1987, tsa. 29
7 Nditulutseni mundende ya mdima+Kuti nditamande dzina lanu.+Chititsani kuti anthu olungama asonkhane ndi kundizungulira,+Chifukwa mumandichitira zabwino.+