Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 119:91
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 91 Ntchito zanu zilipobe mpaka pano chifukwa cha zigamulo zanu,

      Chifukwa zonsezo zimakutumikirani.

  • Yeremiya 31:35, 36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Yehova amene amapereka dzuwa kuti liziwala masana,

      Amene amaika malamulo oti mwezi ndi nyenyezi ziziwala usiku,

      Amene amavundula nyanja

      Kuti mafunde ake achite phokoso,

      Amene dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti:+

      36 “‘Ngati malamulo amenewa angalephere kugwira ntchito yake,

      Ndiye kutinso mbadwa za Isiraeli zingasiye kukhala mtundu, umene umakhala pamaso panga nthawi zonse,’ akutero Yehova.”+

  • Yeremiya 33:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Yehova wanena kuti, ‘Mofanana ndi mmene ndinakhazikitsira pangano langa loti kukhale masana ndi usiku,+ malamulo akumwamba ndi dziko lapansi,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena