Ekisodo 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Mose anatambasula dzanja lake nʼkuloza kumwamba ndi ndodo yake. Atatero, Yehova anachititsa mabingu ndipo anagwetsa matalala ndi moto* padziko lapansi. Choncho Yehova anapitiriza kugwetsa matalala mʼdziko la Iguputo. Salimo 107:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Aona mmene mawu ake amayambitsira mphepo yamkuntho,+Nʼkuchititsa mafunde panyanja. Yesaya 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova adzapangitsa kuti mawu ake aulemerero+ amvekeNdipo adzapangitsa kuti dzanja lake+ limene likutsika ndi mkwiyo waukulu lionekere.+Dzanjalo lidzatsika ndi moto wowononga,+Mvula yamphamvu,+ mphezi komanso mvula yamatalala.+
23 Ndiyeno Mose anatambasula dzanja lake nʼkuloza kumwamba ndi ndodo yake. Atatero, Yehova anachititsa mabingu ndipo anagwetsa matalala ndi moto* padziko lapansi. Choncho Yehova anapitiriza kugwetsa matalala mʼdziko la Iguputo.
30 Yehova adzapangitsa kuti mawu ake aulemerero+ amvekeNdipo adzapangitsa kuti dzanja lake+ limene likutsika ndi mkwiyo waukulu lionekere.+Dzanjalo lidzatsika ndi moto wowononga,+Mvula yamphamvu,+ mphezi komanso mvula yamatalala.+