Salimo 107:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu ayamike Yehova chifukwa cha chikondi chake chokhulupirika,+Ndiponso chifukwa cha ntchito zake zodabwitsa zimene wachitira ana a anthu. Chivumbulutso 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo ankaimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu ndi nyimbo ya Mwanawankhosa+ yakuti: “Ntchito zanu nʼzazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova* Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama komanso zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+
15 Anthu ayamike Yehova chifukwa cha chikondi chake chokhulupirika,+Ndiponso chifukwa cha ntchito zake zodabwitsa zimene wachitira ana a anthu.
3 Iwo ankaimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu ndi nyimbo ya Mwanawankhosa+ yakuti: “Ntchito zanu nʼzazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova* Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama komanso zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+