Salimo 119:137 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 137 Ndinu wolungama, inu Yehova,+Ndipo zigamulo zanu ndi zachilungamo.+ Salimo 119:160 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 160 Mawu anu onse ndi choonadi chokhachokha,+Ndipo zigamulo zanu zonse zolungama zidzakhalapo mpaka kalekale. Chivumbulutso 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako ndinamva guwa lansembe likunena kuti: “Inde, Yehova* Mulungu, inu Wamphamvuyonse,+ ziweruzo* zanu ndi zoona komanso zolungama.”+
160 Mawu anu onse ndi choonadi chokhachokha,+Ndipo zigamulo zanu zonse zolungama zidzakhalapo mpaka kalekale.
7 Kenako ndinamva guwa lansembe likunena kuti: “Inde, Yehova* Mulungu, inu Wamphamvuyonse,+ ziweruzo* zanu ndi zoona komanso zolungama.”+