Salimo 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Adani anga akathawa,+Adzapunthwa nʼkuwonongedwa pamaso panu. Salimo 56:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa tsiku limene ndidzapemphe kuti mundithandize, adani anga adzathawa.+ Mulungu ali kumbali yanga. Sindikukaikira zimenezi.+
9 Pa tsiku limene ndidzapemphe kuti mundithandize, adani anga adzathawa.+ Mulungu ali kumbali yanga. Sindikukaikira zimenezi.+