Salimo 56:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa nthawi imeneyo adani anga adzabwerera pa tsiku limene ndidzaitana inu.+Ndikudziwa bwino kuti Mulungu ali kumbali yanga.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 56:9 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2024, tsa. 6
9 Pa nthawi imeneyo adani anga adzabwerera pa tsiku limene ndidzaitana inu.+Ndikudziwa bwino kuti Mulungu ali kumbali yanga.+