Yesaya 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Aliyense ankauza mnzake kuti: “Woyera, woyera, woyera ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+ Dziko lonse lapansi ladzaza ndi ulemerero wake.” 1 Petulo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma mofanana ndi Woyera amene anakuitanani, inunso khalani oyera mʼmakhalidwe anu onse,+
3 Aliyense ankauza mnzake kuti: “Woyera, woyera, woyera ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+ Dziko lonse lapansi ladzaza ndi ulemerero wake.”