Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kenako Mulungu anati: “Madzi apadziko lapansi akhale pamalo amodzi kuti mtunda uonekere.”+ Ndipo zinaterodi.

  • Yobu 38:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiye ndinati, ‘Ukhoza kufika apa, koma usapitirirepo,

      Ndipo mafunde ako aatali azilekezera pamenepaʼ?+

  • Salimo 136:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Anayala dziko lapansi pamwamba pa madzi,+

      Chifukwa chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.

  • Yeremiya 5:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 ‘Kodi simukuchita nane mantha?’ akutero Yehova.

      ‘Kodi simukunjenjemera pamaso panga?

      Ine ndi amene ndinaika mchenga kuti ukhale malire a nyanja,

      Malire amene adzakhalepo mpaka kalekale.

      Ngakhale kuti mafunde ake amawinduka, sangadutse malirewo.

      Ndipo ngakhale amachita phokoso, sangapitirire malirewo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena