Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Yehova ndi msilikali wamphamvu.+ Dzina lake ndi Yehova.+

  • 1 Samueli 17:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Ndipo onse amene asonkhana panowa adziwa* kuti Yehova sapulumutsa ndi lupanga kapena mkondo,+ chifukwa Yehova ndiye mwini nkhondo,+ ndipo nonsenu akuperekani mʼmanja mwathu.”+

  • 2 Mbiri 20:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Choncho Yahazieli anati: “Tamverani Ayuda nonsenu, anthu a ku Yerusalemu ndi inu Mfumu Yehosafati! Yehova akukuuzani kuti, ‘Musaope kapena kuchita mantha ndi gulu lalikululi chifukwa nkhondoyi si yanu, ndi ya Mulungu.+

  • Yesaya 42:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yehova adzapita kunkhondo ngati munthu wamphamvu.+

      Iye adzachita zinthu modzipereka kwambiri ngati msilikali.+

      Adzafuula, inde adzafuula ngati anthu amene akupita kunkhondo.

      Iye adzasonyeza kuti ndi wamphamvu kwambiri kuposa adani ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena