Yesaya 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu amene amakudalirani ndi mtima wonse* mudzawateteza.Mudzawapatsa mtendere wosatha,+Chifukwa amadalira inu.+
3 Anthu amene amakudalirani ndi mtima wonse* mudzawateteza.Mudzawapatsa mtendere wosatha,+Chifukwa amadalira inu.+