Salimo 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu odziwa dzina lanu adzakukhulupirirani.+Simudzasiya anthu amene amakufunafunani, inu Yehova.+ Yeremiya 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu amene amakhulupirira Yehova komanso amene amadalira Yehova,Ndi amene amadalitsidwa.+
10 Anthu odziwa dzina lanu adzakukhulupirirani.+Simudzasiya anthu amene amakufunafunani, inu Yehova.+