Salimo 111:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chiyambi cha nzeru ndi kuopa Yehova.+ ש [Sin] Onse otsatira malamulo ake amasonyeza kuti ndi ozindikira.+ ת [Taw] Iye ayenera kutamandidwa mpaka kalekale.
10 Chiyambi cha nzeru ndi kuopa Yehova.+ ש [Sin] Onse otsatira malamulo ake amasonyeza kuti ndi ozindikira.+ ת [Taw] Iye ayenera kutamandidwa mpaka kalekale.