-
Yohane 15:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Sindikukutchulaninso kuti akapolo chifukwa kapolo sadziwa zimene mbuye wake amachita. Koma ndakutchulani kuti anzanga, chifukwa ndakudziwitsani zinthu zonse zimene ndamva kwa Atate wanga.
-