Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 15:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Inu Yehova, ndi ndani amene angakhale mlendo mutenti yanu?

      Ndi ndani amene angakhale mʼphiri lanu lopatulika?+

       2 Ndi amene akuyenda mosalakwitsa zinthu,*+

      Amene amachita zinthu zabwino+

      Komanso kulankhula zoona mumtima mwake.+

  • Salimo 24:3, 4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Ndi ndani angakwere kuphiri la Yehova,+

      Ndipo ndi ndani angaime mʼmalo ake opatulika?

       4 Aliyense amene ndi wosalakwa komanso wopanda chinyengo mumtima mwake,+

      Amene sanalumbire mwachinyengo potchula moyo Wanga,*

      Kapena kulumbira pofuna kupusitsa anthu ena.+

  • Salimo 25:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Anthu amene amaopa Yehova ndi amene amakhala naye pa ubwenzi wolimba,+

      Ndipo amawadziwitsa pangano lake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena