Salimo 59:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa cha tchimo lapakamwa pawo ndi mawu a milomo yawo,Ndiponso chifukwa cha mawu otukwana komanso achinyengo amene amalankhula,+ Akodwe ndi kunyada kwawoko. Yeremiya 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mʼnyumba zawo mumveke kuliraMukawabweretsera magulu achifwamba mwadzidzidzi. Chifukwa akumba dzenje kuti andigwireNdipo atchera misampha kuti akole mapazi anga.+
12 Chifukwa cha tchimo lapakamwa pawo ndi mawu a milomo yawo,Ndiponso chifukwa cha mawu otukwana komanso achinyengo amene amalankhula,+ Akodwe ndi kunyada kwawoko.
22 Mʼnyumba zawo mumveke kuliraMukawabweretsera magulu achifwamba mwadzidzidzi. Chifukwa akumba dzenje kuti andigwireNdipo atchera misampha kuti akole mapazi anga.+