Salimo 59:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa cha tchimo la pakamwa pawo, ndi mawu a pamilomo yawo.+Agwidwe chifukwa cha kunyada kwawo,+Chifukwa cha kutukwana ndi chinyengo zimene amachita mobwerezabwereza.
12 Chifukwa cha tchimo la pakamwa pawo, ndi mawu a pamilomo yawo.+Agwidwe chifukwa cha kunyada kwawo,+Chifukwa cha kutukwana ndi chinyengo zimene amachita mobwerezabwereza.