Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 16:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chifukwa simudzandisiya* mʼManda.*+

      Simudzalola kuti wokhulupirika wanu aone dzenje.*+

  • Salimo 28:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ndikuitana inu Yehova, Thanthwe langa,+

      Musatseke makutu anu pamene ine ndikuitana.

      Mukakhala chete pamene ndikukuitanani,

      Ndidzafanana ndi anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+

  • Yesaya 38:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mʼmalo mopeza mtendere ndinali ndi chisoni chachikulu.

      Koma chifukwa chakuti mumandikonda kwambiri,

      Munanditeteza kuti ndisapite kudzenje lachiwonongeko.+

      Machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.*+

  • Yona 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ndinamira mpaka mʼmunsi mwenimweni mwa mapiri.

      Zotsekera za dziko lapansi zinayamba kunditsekereza kuti ndikhale komweko mpaka kalekale.

      Koma inu Yehova Mulungu wanga, munanditulutsa mʼdzenje ndili wamoyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena