Salimo 142:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mvetserani kulira kwanga kopempha thandizo,Chifukwa ndavutika kwambiri. Ndipulumutseni kwa anthu amene akundizunza,+Chifukwa iwo ndi amphamvu kuposa ine.
6 Mvetserani kulira kwanga kopempha thandizo,Chifukwa ndavutika kwambiri. Ndipulumutseni kwa anthu amene akundizunza,+Chifukwa iwo ndi amphamvu kuposa ine.