Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 19:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Usiku umenewo, mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri nʼkukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka mʼmawa, anangoona kuti onse ndi mitembo yokhayokha.+

  • Danieli 6:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mulungu wanga watumiza mngelo wake kudzatseka pakamwa pa mikango+ moti sinandivulaze,+ chifukwa iye sanandipeze ndi mlandu uliwonse ndipo inunso mfumu sindinakulakwireni chilichonse.”

  • Machitidwe 5:18, 19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 nʼkugwira atumwiwo ndipo anawatsekera mʼndende.+ 19 Koma usiku, mngelo wa Yehova* anatsegula zitseko za ndendeyo nʼkuwatulutsa,+ ndipo anawauza kuti:

  • Machitidwe 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma Petulo atayamba kuzindikira zimene zikuchitika anati: “Tsopano ndadziwa kuti Yehova* ndi amene watumiza mngelo wake kudzandipulumutsa mʼmanja mwa Herode komanso ku zinthu zonse zimene Ayuda amayembekezera kuti zichitike.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena