Salimo 145:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova ndi wabwino kwa aliyense,+Ndipo ntchito zake zonse zimasonyeza kuti ndi wachifundo. 1 Timoteyo 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nʼchifukwa chake tikugwira ntchito mwakhama ndiponso mwamphamvu,+ chifukwa chiyembekezo chathu chili mwa Mulungu wamoyo, amene ndi Mpulumutsi+ wa anthu onse, koma makamaka okhulupirika.+
10 Nʼchifukwa chake tikugwira ntchito mwakhama ndiponso mwamphamvu,+ chifukwa chiyembekezo chathu chili mwa Mulungu wamoyo, amene ndi Mpulumutsi+ wa anthu onse, koma makamaka okhulupirika.+