Salimo 73:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa ndinkachitira nsanje anthu onyada*Ndikamaona mtendere wa anthu oipa.+ Miyambo 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mtima wako usamasirire anthu ochimwa,+Koma iwe uziopa Yehova tsiku lonse.+