Salimo 37:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova amadziwa mavuto amene anthu osalakwa akukumana nawo,*Ndipo cholowa chawo chidzakhalapo mpaka kalekale.+ Yeremiya 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma inu Yehova, mukundidziwa bwino+ ndipo mumandiona.Mwafufuza mtima wanga ndipo mwapeza kuti ndine wokhulupirika kwa inu.+ Apatuleni ngati nkhosa zimene zikukaphedwa,Ndipo muwaike padera poyembekezera tsiku limene adzaphedwe. 1 Petulo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Maso a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva mapemphero awo opembedzera,+ koma Yehova* amakwiyira anthu amene amachita zoipa.”+
18 Yehova amadziwa mavuto amene anthu osalakwa akukumana nawo,*Ndipo cholowa chawo chidzakhalapo mpaka kalekale.+
3 Koma inu Yehova, mukundidziwa bwino+ ndipo mumandiona.Mwafufuza mtima wanga ndipo mwapeza kuti ndine wokhulupirika kwa inu.+ Apatuleni ngati nkhosa zimene zikukaphedwa,Ndipo muwaike padera poyembekezera tsiku limene adzaphedwe.
12 Maso a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva mapemphero awo opembedzera,+ koma Yehova* amakwiyira anthu amene amachita zoipa.”+