Salimo 62:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Ndithudi, ndikuyembekezera* Mulungu modekha. Chipulumutso changa chimachokera kwa iye.+ Maliro 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndi bwino kuti munthu akhale chete*+ nʼkumayembekezera chipulumutso cha Yehova.+