-
1 Samueli 25:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Davide atamva kuti Nabala wamwalira ananena kuti: “Adalitsike Yehova amene wandiweruzira mlandu+ wa mawu onyoza a Nabala,+ komanso wandiletsa ine mtumiki wake kuti ndisachite choipa chilichonse.+ Yehova wabwezera zoipa za Nabala pamutu pake!” Kenako Davide anatuma anthu kuti akamufunsirire Abigayeli kuti akhale mkazi wake.
-
-
Salimo 52:4, 5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Umakonda mawu onse opweteka ena,
Iwe amene lilime lako limalankhula zachinyengo.
-