Salimo 34:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mavuto* a munthu wolungama ndi ambiri,+Koma Yehova amamupulumutsa ku mavuto onsewo.+ Miyambo 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa munthu wolungama akhoza kugwa maulendo 7 ndipo adzadzukanso,+Koma anthu oipa adzakumana ndi tsoka ndipo adzagwa.+
16 Chifukwa munthu wolungama akhoza kugwa maulendo 7 ndipo adzadzukanso,+Koma anthu oipa adzakumana ndi tsoka ndipo adzagwa.+