21 Nthawi yomweyo Danieli anayankha mfumuyo kuti: “Inu mfumu, mukhale ndi moyo mpaka kalekale. 22 Mulungu wanga watumiza mngelo wake kudzatseka pakamwa pa mikango+ moti sinandivulaze,+ chifukwa iye sanandipeze ndi mlandu uliwonse ndipo inunso mfumu sindinakulakwireni chilichonse.”