Salimo 91:11, 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa adzalamula angelo ake+ zokhudza iwe,Kuti akuteteze mʼnjira zako zonse.+ 12 Iwo adzakunyamula mʼmanja mwawo,+Kuti phazi lako lisawombe mwala.+
11 Chifukwa adzalamula angelo ake+ zokhudza iwe,Kuti akuteteze mʼnjira zako zonse.+ 12 Iwo adzakunyamula mʼmanja mwawo,+Kuti phazi lako lisawombe mwala.+