Yesaya 63:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa nthawi yonse imene iwo ankavutika, iye ankavutikanso.+ Ndipo mthenga wake* anawapulumutsa.+ Iye anawawombola chifukwa cha chikondi komanso chifundo chake,+Ndipo nthawi zonse ankawakweza mʼmwamba komanso kuwanyamula.+
9 Pa nthawi yonse imene iwo ankavutika, iye ankavutikanso.+ Ndipo mthenga wake* anawapulumutsa.+ Iye anawawombola chifukwa cha chikondi komanso chifundo chake,+Ndipo nthawi zonse ankawakweza mʼmwamba komanso kuwanyamula.+