Salimo 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Makolo athu ankadalira inu.+Iwo ankakudalirani ndipo inu munkawapulumutsa.+ Danieli 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngati mungatiponyere mungʼanjo yoyaka moto, Mulungu wathu amene tikumutumikira akhoza kutipulumutsa. Iye akhozanso kutipulumutsa mʼmanja mwanu mfumu.+ Danieli 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mfumu inasangalala kwambiri ndipo inalamula kuti Danieli amutulutse mʼdzenjemo. Danieli anatulutsidwadi mʼdzenjemo ndipo sanavulale paliponse chifukwa anakhulupirira Mulungu wake.+
17 Ngati mungatiponyere mungʼanjo yoyaka moto, Mulungu wathu amene tikumutumikira akhoza kutipulumutsa. Iye akhozanso kutipulumutsa mʼmanja mwanu mfumu.+
23 Mfumu inasangalala kwambiri ndipo inalamula kuti Danieli amutulutse mʼdzenjemo. Danieli anatulutsidwadi mʼdzenjemo ndipo sanavulale paliponse chifukwa anakhulupirira Mulungu wake.+