Ezara 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ndinanena kuti: “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi kuti ndikweze nkhope yanga kuyangʼana kwa inu Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu zachuluka kupitirira pamutu pathu ndipo machimo athu aunjikana mpaka kumwamba.+ Salimo 40:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Masoka amene andizungulira ndi ambiri moti sindingathe kuwawerenga.+ Zolakwa zanga ndi zochuluka moti sindikutha kuona kumene ndikulowera.+Zachuluka kwambiri kuposa tsitsi lakumutu kwanga,Ndipo ndataya mtima.
6 Kenako ndinanena kuti: “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi kuti ndikweze nkhope yanga kuyangʼana kwa inu Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu zachuluka kupitirira pamutu pathu ndipo machimo athu aunjikana mpaka kumwamba.+
12 Masoka amene andizungulira ndi ambiri moti sindingathe kuwawerenga.+ Zolakwa zanga ndi zochuluka moti sindikutha kuona kumene ndikulowera.+Zachuluka kwambiri kuposa tsitsi lakumutu kwanga,Ndipo ndataya mtima.