Salimo 54:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Taonani! Mulungu ndi amene amandithandiza.+Yehova amadalitsa anthu amene akundithandiza. Yesaya 50:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzandithandiza.+ Nʼchifukwa chake sindidzamva kuti ndanyozeka. Nʼchifukwa chake ndalimbitsa nkhope yanga ngati mwala wa nsangalabwi,+Ndipo ndikudziwa kuti sindidzachititsidwa manyazi. Aheberi 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tikhale olimba mtima ndithu ndipo tinene kuti: “Yehova* ndi amene amandithandiza. Sindidzaopa. Munthu angandichite chiyani?”+
7 Koma Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzandithandiza.+ Nʼchifukwa chake sindidzamva kuti ndanyozeka. Nʼchifukwa chake ndalimbitsa nkhope yanga ngati mwala wa nsangalabwi,+Ndipo ndikudziwa kuti sindidzachititsidwa manyazi.
6 Tikhale olimba mtima ndithu ndipo tinene kuti: “Yehova* ndi amene amandithandiza. Sindidzaopa. Munthu angandichite chiyani?”+