Salimo 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kukhala wokhulupirika komanso kuchita zinthu zoyenera kunditeteze,+Chifukwa chiyembekezo changa chili mwa inu.+ Miyambo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu owongoka mtima, amawasungira nzeru zopindulitsa.Iye ndi chishango kwa anthu amene amachita zinthu mokhulupirika.+
21 Kukhala wokhulupirika komanso kuchita zinthu zoyenera kunditeteze,+Chifukwa chiyembekezo changa chili mwa inu.+
7 Anthu owongoka mtima, amawasungira nzeru zopindulitsa.Iye ndi chishango kwa anthu amene amachita zinthu mokhulupirika.+