Salimo 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?+ Nʼchifukwa chiyani mukuchedwa kundipulumutsa?Nʼchifukwa chiyani simukumva kubuula kwanga?+ Yohane 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Moyo wanga ukuvutika tsopano,+ kodi ndinene chiyani? Atate ndipulumutseni ku nthawi yovutayi.+ Komabe nthawi imeneyi ikuyenera kundifikira pakuti nʼchifukwa chake ndinabwera.
22 Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?+ Nʼchifukwa chiyani mukuchedwa kundipulumutsa?Nʼchifukwa chiyani simukumva kubuula kwanga?+
27 Moyo wanga ukuvutika tsopano,+ kodi ndinene chiyani? Atate ndipulumutseni ku nthawi yovutayi.+ Komabe nthawi imeneyi ikuyenera kundifikira pakuti nʼchifukwa chake ndinabwera.