Salimo 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adani anga andizungulira ngati agalu.+Andizungulira ngati gulu la anthu ochita zoipa,+Mofanana ndi mkango, iwo akundiluma manja ndi mapazi.+ Mateyu 27:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Cha mʼma 3 kolokomo, Yesu anafuula mwamphamvu kuti: “Eʹli, Eʹli, laʹma sa·bach·thaʹni?” kutanthauza kuti, “Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?”+ Maliko 15:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Cha mʼma 3 kolokomo, Yesu anafuula mwamphamvu kuti: “Eʹli, Eʹli, laʹma sa·bach·thaʹni?” Mawu amenewa akawamasulira amatanthauza kuti: “Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?”+
16 Adani anga andizungulira ngati agalu.+Andizungulira ngati gulu la anthu ochita zoipa,+Mofanana ndi mkango, iwo akundiluma manja ndi mapazi.+
46 Cha mʼma 3 kolokomo, Yesu anafuula mwamphamvu kuti: “Eʹli, Eʹli, laʹma sa·bach·thaʹni?” kutanthauza kuti, “Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?”+
34 Cha mʼma 3 kolokomo, Yesu anafuula mwamphamvu kuti: “Eʹli, Eʹli, laʹma sa·bach·thaʹni?” Mawu amenewa akawamasulira amatanthauza kuti: “Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?”+